Surah Al-Asr — The Declining Day, Epoch
Surah Al-Asr (The Declining Day, Epoch) is chapter 103 of the Quran, with 3 verses. This page presents the Arabic text with a Chichewa translation, verse by verse.
وَٱلۡعَصۡرِ
Pali nthawi
Ayah 1إِنَّ ٱلۡإِنسَٰنَ لَفِي خُسۡرٍ
Ndithudi ! Munthu ndi otayika
Ayah 2إِلَّا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ وَتَوَاصَوۡاْ بِٱلۡحَقِّ وَتَوَاصَوۡاْ بِٱلصَّبۡرِ
Kupatula okhawo amene amakhulupirira ndi kuchita ntchito zabwino ndipo amalimbikitsana wina ndi mzake kuchita chilungamo ndi kukumbutsana kupirira
Ayah 3