Surah Al-Aadiyaat — The Chargers

Surah Al-Aadiyaat (The Chargers) is chapter 100 of the Quran, with 11 verses. This page presents the Arabic text with a Chichewa translation, verse by verse.

وَٱلۡعَٰدِيَٰتِ ضَبۡحࣰ ا

Palizothamangakwambirindikupumakwawokofulumira

Ayah 1

فَٱلۡمُورِيَٰتِ قَدۡحࣰ ا

Ndi zimene zimaonetsa moto zikamathamanga

Ayah 2

فَٱلۡمُغِيرَٰتِ صُبۡحࣰ ا

Ndipo zimachita nkhondo m’mbandakucha

Ayah 3

فَأَثَرۡنَ بِهِۦ نَقۡعࣰ ا

Ndi kuonetsa fumbi

Ayah 4

فَوَسَطۡنَ بِهِۦ جَمۡعًا

Ndi kuphwanya pakati gulu la adani

Ayah 5

إِنَّ ٱلۡإِنسَٰنَ لِرَبِّهِۦ لَكَنُودࣱ‏

Ndithudi! Munthu sathokoza kwaAmbuye wake

Ayah 6

وَإِنَّهُۥ عَلَىٰ ذَٰلِكَ لَشَهِيدࣱ‏

Ndipo mwini wake amachitira umboni zimenezi

Ayah 7

وَإِنَّهُۥ لِحُبِّ ٱلۡخَيۡرِ لَشَدِيدٌ

Ndithudi iye ali kukonda chuma kwambiri

Ayah 8

۞أَفَلَا يَعۡلَمُ إِذَا بُعۡثِرَ مَا فِي ٱلۡقُبُورِ

Kodi iye sadziwa kuti pamene zonse zili m’manda zidzatulutsidwa ndi kuonetsedwa poyera

Ayah 9

وَحُصِّلَ مَا فِي ٱلصُّدُورِ

Ndizonsezimenezilim’mitimayaanthuzizidzaululidwa

Ayah 10

إِنَّ رَبَّهُم بِهِمۡ يَوۡمَئِذࣲ لَّخَبِيرُۢ

Ndithudi, patsiku limeneli, Ambuye wako adzakhala ali kudziwa chilichonse

Ayah 11