Surah Al-Falaq — The Dawn
Surah Al-Falaq (The Dawn) is chapter 113 of the Quran, with 5 verses. This page presents the Arabic text with a Chichewa translation, verse by verse.
قُلۡ أَعُوذُ بِرَبِّ ٱلۡفَلَقِ
Nena: “Ine ndifuna kuthawira kwa Ambuye wa M’mbandakucha
Ayah 1مِن شَرِّ مَا خَلَقَ
Kuchokera ku zinthu zonyansa zimene walenga
Ayah 2وَمِن شَرِّ غَاسِقٍ إِذَا وَقَبَ
Ndi kuchokera ku zonyansa za nthawi ya usiku pamene mdima ufika
Ayah 3وَمِن شَرِّ ٱلنَّفَّٰثَٰتِ فِي ٱلۡعُقَدِ
Ndi kuchokera ku zonyansa za anthu a matsenga pamene auzila pfundo
Ayah 4وَمِن شَرِّ حَاسِدٍ إِذَا حَسَدَ
“Ndi ku zonyansa za munthu wa dumbo pamene achita nsanje.”
Ayah 5