Surah An-Naas — Mankind
Surah An-Naas (Mankind) is chapter 114 of the Quran, with 6 verses. This page presents the Arabic text with a Chichewa translation, verse by verse.
قُلۡ أَعُوذُ بِرَبِّ ٱلنَّاسِ
Nena: “Ine ndifuna kuthawira kwa Ambuye wa anthu
Ayah 1مَلِكِ ٱلنَّاسِ
Mfumu ya anthu
Ayah 2إِلَٰهِ ٱلنَّاسِ
Mulungu wa anthu
Ayah 3مِن شَرِّ ٱلۡوَسۡوَاسِ ٱلۡخَنَّاسِ
Kuchokera ku zonyansa za kazitape amene amachoka akatha
Ayah 4ٱلَّذِي يُوَسۡوِسُ فِي صُدُورِ ٱلنَّاسِ
Amene amanong’oneza m’mitima mwa anthu
Ayah 5مِنَ ٱلۡجِنَّةِ وَٱلنَّاسِ
Ya majini ndi anthu.”
Ayah 6